Oweruza 9:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Ndipo zoipa zonse za amuna a m’Sekemu, Mulungu anachititsa kuti ziwabwerere pamutu pawo, kuti temberero+ la Yotamu+ mwana wa Yerubaala,+ liwagwere.+ 1 Mafumu 2:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Ndiyeno mfumuyo inapitiriza kuuza Simeyi kuti: “Iweyo wekha ukudziwa bwino mumtima mwako zoipa zonse zimene unachitira Davide bambo anga.+ Yehova akubwezera ndithu pamutu pako zoipa zimene unachita.+ Salimo 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mavuto ake adzabwerera pamutu pake,+Ndipo chiwawa chake chidzatsikira paliwombo pake.+
57 Ndipo zoipa zonse za amuna a m’Sekemu, Mulungu anachititsa kuti ziwabwerere pamutu pawo, kuti temberero+ la Yotamu+ mwana wa Yerubaala,+ liwagwere.+
44 Ndiyeno mfumuyo inapitiriza kuuza Simeyi kuti: “Iweyo wekha ukudziwa bwino mumtima mwako zoipa zonse zimene unachitira Davide bambo anga.+ Yehova akubwezera ndithu pamutu pako zoipa zimene unachita.+