Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 9:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Yehova wanena kuti, “Taona masiku akubwera ndipo ndidzaimba mlandu aliyense wodulidwa koma amene sanachite mdulidwe wa mtima wake.+

  • Yeremiya 25:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Taonani! Tsoka likuyenda kuchokera mu mtundu wina kupita mu mtundu wina,+ ndipo mkuntho wamphamvu udzafika kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+

  • Yeremiya 49:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Yehova wanena kuti: “Taonani! Ngakhale kuti sanazolowere kumwa za m’kapu, iwo adzamwa ndithu.+ Kodi iwe udzasiyidwa osapatsidwa chilango? Ayi, sudzasiyidwa osapatsidwa chilango pakuti udzamwa ndithu za m’kapumo.”+

  • Yoweli 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Makamu ambirimbiri a anthu ali m’chigwa+ choweruzira mlandu, pakuti tsiku la Yehova layandikira m’chigwa choweruzira mlandu.+

  • Mika 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndidzabwezera mokwiya ndiponso mwaukali mitundu ya anthu imene sinandimvere.”+

  • 2 Petulo 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Komabe, tsiku la Yehova+ lidzafika ngati mbala,+ pamene kumwamba kudzachoka+ ndi mkokomo waukulu,+ koma zinthu zimene zimapanga kumwamba ndi dziko lapansi zidzatentha kwambiri n’kusungunuka,+ ndipo dziko lapansi+ ndi ntchito zake zidzaonekera poyera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena