Yesaya 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti Yehova wakwiyira mitundu yonse.+ Wapsera mtima asilikali awo onse.+ Iye awawononga ndipo awapha.+ Yeremiya 25:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho ndinatenga chikho chija chimene chinali m’dzanja la Yehova ndipo ndinamwetsa mitundu yonse imene Yehova ananditumizako.+
2 Pakuti Yehova wakwiyira mitundu yonse.+ Wapsera mtima asilikali awo onse.+ Iye awawononga ndipo awapha.+
17 Choncho ndinatenga chikho chija chimene chinali m’dzanja la Yehova ndipo ndinamwetsa mitundu yonse imene Yehova ananditumizako.+