Amosi 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ‘Pa mabanja onse apadziko lapansi+ ine ndimadziwa inu nokha.+ Choncho ndidzakulangani chifukwa cha zolakwa zanu zonse.+ Machitidwe 7:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 “Anthu okanika inu ndi osachita mdulidwe wa mumtima+ ndi m’makutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mmene anachitira makolo anu inunso mukuchita chimodzimodzi.+ Aroma 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pajatu mdulidwe+ ndi waphindu pokhapokha ngati iweyo umatsatiradi chilamulo.+ Koma ngati umaphwanya chilamulo, ndiye kuti mdulidwe+ wako ndi wopanda tanthauzo.+
2 ‘Pa mabanja onse apadziko lapansi+ ine ndimadziwa inu nokha.+ Choncho ndidzakulangani chifukwa cha zolakwa zanu zonse.+
51 “Anthu okanika inu ndi osachita mdulidwe wa mumtima+ ndi m’makutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mmene anachitira makolo anu inunso mukuchita chimodzimodzi.+
25 Pajatu mdulidwe+ ndi waphindu pokhapokha ngati iweyo umatsatiradi chilamulo.+ Koma ngati umaphwanya chilamulo, ndiye kuti mdulidwe+ wako ndi wopanda tanthauzo.+