1 Samueli 25:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Komabe, pali Yehova Mulungu wamoyo wa Isiraeli, amene wandigwira kuti ndisakuchitire choipa,+ ukanapanda kufulumira kudzakumana nane,+ ndithu sipakanatsala munthu wokodzera khoma+ m’banja la Nabala pofika mawa m’mawa.”
34 Komabe, pali Yehova Mulungu wamoyo wa Isiraeli, amene wandigwira kuti ndisakuchitire choipa,+ ukanapanda kufulumira kudzakumana nane,+ ndithu sipakanatsala munthu wokodzera khoma+ m’banja la Nabala pofika mawa m’mawa.”