Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 27:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Yembekezera Yehova.+ Limba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu.+

      Yembekezera Yehova.+

  • Salimo 37:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Yembekezera Yehova, ndi kusunga njira zake,+

      Ndipo adzakukweza kuti ulandire dziko lapansi.+

      Pamene oipa akuphedwa, iwe udzaona.+

  • Salimo 62:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 62 Ndithudi, moyo wanga ukuyembekezera Mulungu modekha.+

      Chipulumutso changa chidzachokera kwa iye.+

  • Salimo 130:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Isiraeli ayembekezere Yehova,+

      Pakuti Yehova amasonyeza kukoma mtima kosatha.+

      Iye ali ndi mphamvu zochuluka zowombolera anthu ake.+

  • Miyambo 20:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Usanene kuti: “Ndidzabwezera choipa.”+ Khulupirira Yehova+ ndipo iye adzakupulumutsa.+

  • Yesaya 30:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Chotero Yehova azidzayembekezera kuti akukomereni mtima+ ndipo adzanyamuka kuti akuchitireni chifundo,+ pakuti Yehova ndi Mulungu amene amaweruza mwachilungamo.+ Odala+ ndi anthu onse amene amamuyembekezera.+

  • Yakobo 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Choncho lezani mtima abale, kufikira kukhalapo*+ kwa Ambuye. Ganizirani mmene amachitira mlimi. Iye amayembekezerabe zipatso zofunika kwambiri zotuluka m’nthaka. Amakhala wodekha mpaka itagwa mvula yoyamba ndi mvula yomaliza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena