Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Kubwezera ndi kwanga, chilangonso ndi changa.+

      Pa nthawi yoikidwiratu phazi lawo lidzaterereka poyenda,+

      Pakuti tsiku la tsoka lawo layandikira,+

      Ndipo zowagwera zikufika mofulumira.’+

  • Miyambo 24:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Usanene kuti: “Ndim’chitira zimene iye anandichitira.+ Aliyense ndizim’bwezera mogwirizana ndi zimene anachita.”+

  • Mateyu 5:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 “Inu munamva kuti anati, ‘Diso kulipira diso, ndi dzino kulipira dzino.’+

  • Aroma 12:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Musabwezere choipa pa choipa.+ Chitani zimene anthu onse amaziona kuti ndi zabwino.

  • 1 Atesalonika 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Onetsetsani kuti wina asabwezere choipa pa choipa kwa wina aliyense,+ koma nthawi zonse yesetsani kuchita zabwino kwa okhulupirira anzanu ndi kwa ena onse.+

  • 1 Petulo 3:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Osabwezera choipa pa choipa+ kapena chipongwe pa chipongwe,+ koma m’malomwake muzidalitsa,+ chifukwa anakuitanirani njira ya moyo imeneyi, kuti mudzalandire dalitso.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena