Miyambo 20:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Usanene kuti: “Ndidzabwezera choipa.”+ Khulupirira Yehova+ ndipo iye adzakupulumutsa.+ Aroma 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musabwezere choipa pa choipa.+ Chitani zimene anthu onse amaziona kuti ndi zabwino. 1 Atesalonika 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Onetsetsani kuti wina asabwezere choipa pa choipa kwa wina aliyense,+ koma nthawi zonse yesetsani kuchita zabwino kwa okhulupirira anzanu ndi kwa ena onse.+
15 Onetsetsani kuti wina asabwezere choipa pa choipa kwa wina aliyense,+ koma nthawi zonse yesetsani kuchita zabwino kwa okhulupirira anzanu ndi kwa ena onse.+