2 Samueli 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwina Yehova aona+ ndi diso lake, ndipo lero Yehova abwezeretsa kwa ine zinthu zabwino m’malo mwa temberero la Simeyi.”+ Salimo 34:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mngelo wa Yehova amamanga msasa mozungulira onse oopa Mulungu,+Ndipo amawapulumutsa.+ 1 Petulo 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho amene akuvutika mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu, aike miyoyo yawo m’manja mwa Mlengi wokhulupirika, pamene akupitiriza kuchita zabwino.+
12 Mwina Yehova aona+ ndi diso lake, ndipo lero Yehova abwezeretsa kwa ine zinthu zabwino m’malo mwa temberero la Simeyi.”+
19 Choncho amene akuvutika mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu, aike miyoyo yawo m’manja mwa Mlengi wokhulupirika, pamene akupitiriza kuchita zabwino.+