Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 29:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Kenako Leya anakhala ndi pakati n’kubereka mwana wamwamuna. Mwanayo anamutcha Rubeni,*+ popeza anati: “N’chifukwa chakuti Yehova waona kusautsika kwanga,+ ndipo tsopano mwamuna wanga ayamba kundikonda kwambiri.”

  • Ekisodo 2:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Choncho Mulungu anayang’ana ana a Isiraeli ndipo anaona kuvutika kwawo.

  • Ekisodo 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Yehova anawonjezeranso kuti: “Ndaona nsautso ya anthu anga amene ali ku Iguputo, ndipo ndamva kulira kwawo chifukwa cha amene akuwagwiritsa ntchito mwankhanza. Zoonadi, ndikudziwa bwino zowawa zawo.+

  • Salimo 25:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Onani masautso anga ndi mavuto anga,+

      Ndipo mundichotsere machimo anga onse.+

  • Miyambo 15:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Maso a Yehova ali paliponse.+ Amayang’ana anthu oipa ndi abwino omwe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena