2 Samueli 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwina Yehova aona+ ndi diso lake, ndipo lero Yehova abwezeretsa kwa ine zinthu zabwino m’malo mwa temberero la Simeyi.”+ Salimo 119:153 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 153 Onani kusautsika kwanga ndipo ndipulumutseni,+Pakuti sindinaiwale chilamulo chanu.+
12 Mwina Yehova aona+ ndi diso lake, ndipo lero Yehova abwezeretsa kwa ine zinthu zabwino m’malo mwa temberero la Simeyi.”+