Genesis 30:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Leya anati: “Mulungu wandipatsadi mphoto yabwino. Tsopano mwamuna wanga ayamba kukondwera nane,+ chifukwa ndam’berekera ana aamuna 6.”+ Chotero Leya anatcha mwanayo dzina lakuti Zebuloni.*+ 1 Samueli 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mkazi mnzake wa Hana anali kum’sautsa+ kwambiri n’cholinga choti amukhumudwitse, chifukwa chakuti Yehova anali atatseka mimba yake. Luka 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Izitu n’zimene Yehova wandichitira masiku ano pamene wandicheukira kuti andichotsere chitonzo pamaso pa anthu.”+
20 Ndiyeno Leya anati: “Mulungu wandipatsadi mphoto yabwino. Tsopano mwamuna wanga ayamba kukondwera nane,+ chifukwa ndam’berekera ana aamuna 6.”+ Chotero Leya anatcha mwanayo dzina lakuti Zebuloni.*+
6 Mkazi mnzake wa Hana anali kum’sautsa+ kwambiri n’cholinga choti amukhumudwitse, chifukwa chakuti Yehova anali atatseka mimba yake.
25 “Izitu n’zimene Yehova wandichitira masiku ano pamene wandicheukira kuti andichotsere chitonzo pamaso pa anthu.”+