Salimo 29:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Liwu la Yehova lili pamwamba pa madzi,*+Liwu la Mulungu waulemerero+ lagunda ngati bingu.+Yehova ali pamwamba pa madzi ambiri.+ Ezekieli 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Phokoso la mapiko a akerubiwo+ linali kumveka mpaka kubwalo lakunja. Phokosolo linali kumveka ngati kulankhula kwa Mulungu Wamphamvuyonse.+ Chivumbulutso 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mapazi ake anali ngati mkuwa woyengedwa+ bwino ukamanyezimira m’ng’anjo, ndipo mawu+ ake anali ngati mkokomo wa madzi ambiri.
3 Liwu la Yehova lili pamwamba pa madzi,*+Liwu la Mulungu waulemerero+ lagunda ngati bingu.+Yehova ali pamwamba pa madzi ambiri.+
5 Phokoso la mapiko a akerubiwo+ linali kumveka mpaka kubwalo lakunja. Phokosolo linali kumveka ngati kulankhula kwa Mulungu Wamphamvuyonse.+
15 Mapazi ake anali ngati mkuwa woyengedwa+ bwino ukamanyezimira m’ng’anjo, ndipo mawu+ ake anali ngati mkokomo wa madzi ambiri.