Deuteronomo 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi moto wowononga,+ iye ndi Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha basi.*+ Salimo 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzavumbitsira oipa misampha, moto ndi sulufule,+Komanso mphepo yotentha, monga gawo limene ayenera kumwa.+ Salimo 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mudzawakhalitsa ngati oponyedwa mung’anjo yamoto pa nthawi ya kuonekera kwanu.+Yehova adzawameza mu mkwiyo wake, ndipo moto udzawanyeketsa.+ Salimo 97:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Patsogolo pake pakuyaka moto,+Ndipo ukupsereza adani ake onse omuzungulira.+
24 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi moto wowononga,+ iye ndi Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha basi.*+
6 Iye adzavumbitsira oipa misampha, moto ndi sulufule,+Komanso mphepo yotentha, monga gawo limene ayenera kumwa.+
9 Mudzawakhalitsa ngati oponyedwa mung’anjo yamoto pa nthawi ya kuonekera kwanu.+Yehova adzawameza mu mkwiyo wake, ndipo moto udzawanyeketsa.+