Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pakuti pa kukwiya kwanga moto wayaka,+

      Ndipo udzayaka mpaka kukafika ku Manda,* malo a pansi penipeni.+

      Udzanyeketsa dziko lapansi ndi zipatso zake,+

      Ndi kuyatsa maziko a mapiri.+

  • Yesaya 34:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pakuti Yehova wakwiyira mitundu yonse.+ Wapsera mtima asilikali awo onse.+ Iye awawononga ndipo awapha.+

  • Ezekieli 36:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mawu amene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena ndi akuti, ‘Ndithudi, ndidzadzudzula anthu otsala a mitundu ina ndiponso Edomu yense nditakwiya kwambiri.+ Ndidzadzudzula amene anatenga dziko langa kuti likhale lawo. Iwo analitenga akusangalala+ komanso kunyoza mumtima mwawo+ poona kuti atenga dzikolo ndi malo ake odyetserako ziweto.’”’+

  • Zefaniya 1:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Siliva kapena golide wawo sadzawapulumutsa pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+ Moto wa mkwiyo wake udzanyeketsa dziko lonse lapansi,+ chifukwa iye adzafafaniza anthu onse okhala padziko lapansi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena