Ekisodo 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Adzaopa ndipo adzagwidwa ndi mantha aakulu.+Chifukwa cha dzanja lanu lamphamvu, adzakhala chete ngati mwala.Kufikira anthu anu+ atadutsa, inu Yehova,Kufikira anthu anu amene munawapanga+ atadutsa.+ Salimo 98:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 98 IMBIRANI Yehova nyimbo yatsopano,+Pakuti zimene wachita ndi zodabwitsa.+Dzanja lake lamanja, ndithu mkono wake woyera, wabweretsa chipulumutso.+ Yesaya 53:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Kodi ndani wakhulupirira zimene ife tamva?+ Ndipo kodi dzanja la Yehova+ laonetsedwa kwa ndani?+ Luka 1:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Wachita zamphamvu ndi dzanja lake,+ wabalalitsira kutali odzikweza m’zolinga za mitima yawo.+
16 Adzaopa ndipo adzagwidwa ndi mantha aakulu.+Chifukwa cha dzanja lanu lamphamvu, adzakhala chete ngati mwala.Kufikira anthu anu+ atadutsa, inu Yehova,Kufikira anthu anu amene munawapanga+ atadutsa.+
98 IMBIRANI Yehova nyimbo yatsopano,+Pakuti zimene wachita ndi zodabwitsa.+Dzanja lake lamanja, ndithu mkono wake woyera, wabweretsa chipulumutso.+