Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 20:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chonde mutilole tidzere m’dziko lanu. Sitidzera m’munda wanu uliwonse, kapena m’munda wa mpesa uliwonse. Sitimwa madzi a pachitsime chanu chilichonse. Tizingoyenda+ mumsewu wa mfumu, osapatukira kudzanja lamanja kapena lamanzere,+ mpaka titadutsa m’dziko lanu.’”

  • Numeri 21:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “Tiloleni tidzere m’dziko lanu. Sitipatukira pamunda uliwonse, kapena pamunda wa mpesa. Sitimwa madzi pachitsime chilichonse. Tizingoyenda mumsewu wa mfumu mpaka titadutsa m’dziko lanu.”+

  • Deuteronomo 2:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 ‘Ndilole ndidutse m’dziko lako. Ndidzangodutsa mumsewu. Sindidzatembenukira kudzanja lamanja kapena lamanzere.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena