Numeri 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Tiloleni tidzere m’dziko lanu. Sitipatukira pamunda uliwonse, kapena pamunda wa mpesa. Sitimwa madzi pachitsime chilichonse. Tizingoyenda mumsewu wa mfumu mpaka titadutsa m’dziko lanu.”+ Oweruza 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Kenako Aisiraeli anatumiza mithenga kwa Sihoni mfumu ya Aamori, ya ku Hesiboni,+ kuti: “Tiloleni tidutse m’dziko lanu kupita kumalo athu.”+
22 “Tiloleni tidzere m’dziko lanu. Sitipatukira pamunda uliwonse, kapena pamunda wa mpesa. Sitimwa madzi pachitsime chilichonse. Tizingoyenda mumsewu wa mfumu mpaka titadutsa m’dziko lanu.”+
19 “‘Kenako Aisiraeli anatumiza mithenga kwa Sihoni mfumu ya Aamori, ya ku Hesiboni,+ kuti: “Tiloleni tidutse m’dziko lanu kupita kumalo athu.”+