2 Samueli 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anayamba kuponya mivi kuti awabalalitse.+Anaponya mphezi kuti awasokoneze.+ Yobu 36:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Iye wafumbata mphezi m’manja mwake,Ndipo amailamula kuti igwere woukira.+ Salimo 144:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ng’animitsani mphezi kuti muwabalalitse.+Tumizani mivi yanu kuti muwasokoneze.+