Yobu 36:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Iye amafumbata mphezi mʼmanja mwake,Ndipo amailamula kuti ikagwere pamene akufuna.+