Deuteronomo 32:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndidzaledzeretsa mivi yanga ndi magazi,+Magazi a anthu ophedwa ndi ogwidwa.Ndipo lupanga langa lidzadya nyama,+Pamodzi ndi mitu ya atsogoleri a adani.’+ Salimo 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu mudzawachititsa kutembenuka ndi kuthawa.+Mudzachita zimenezi ndi zingwe za mauta amene mwakonzekera kuwalasa nawo pankhope.+ Salimo 45:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mivi yako yakuthwa idzalasa mitima ya adani a mfumu,+Mitundu ya anthu idzagwa pamapazi ako.+
42 Ndidzaledzeretsa mivi yanga ndi magazi,+Magazi a anthu ophedwa ndi ogwidwa.Ndipo lupanga langa lidzadya nyama,+Pamodzi ndi mitu ya atsogoleri a adani.’+
12 Inu mudzawachititsa kutembenuka ndi kuthawa.+Mudzachita zimenezi ndi zingwe za mauta amene mwakonzekera kuwalasa nawo pankhope.+