Salimo 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye adzadzikonzera zida za imfa,+Ndipo adzapanga mivi yake kukhala yoyaka moto walawilawi.+ Salimo 77:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mitambo yatulutsa mabingu ndi kugwetsa madzi.+Thambo latulutsa mkokomo.Mphezi zanu zinawala paliponse ngati mivi.+
17 Mitambo yatulutsa mabingu ndi kugwetsa madzi.+Thambo latulutsa mkokomo.Mphezi zanu zinawala paliponse ngati mivi.+