Salimo 68:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Vomerezani kuti Mulungu ndi wamphamvu zochuluka.+Iye akulamulira Isiraeli ndipo mphamvu zake zili m’mitambo.+ Salimo 150:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 150 Tamandani Ya, anthu inu!+Tamandani Mulungu m’malo ake oyera.+Mutamandeni m’mlengalenga mmene mumasonyeza mphamvu zake.+
34 Vomerezani kuti Mulungu ndi wamphamvu zochuluka.+Iye akulamulira Isiraeli ndipo mphamvu zake zili m’mitambo.+
150 Tamandani Ya, anthu inu!+Tamandani Mulungu m’malo ake oyera.+Mutamandeni m’mlengalenga mmene mumasonyeza mphamvu zake.+