Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 13:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Yehova anali kuyenda patsogolo pawo mumtambo woima njo ngati chipilala powatsogolera usana,+ ndipo usiku anali kuwatsogolera m’moto woima njo ngati chipilala kuti uziwaunikira, kuti apitirizebe ulendo usana ndi usiku.+

  • Salimo 104:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Mwadzifunditsa kuwala ngati chofunda,+

      Mwatambasula kumwamba ngati nsalu ya chihema.+

  • Yesaya 60:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Dzuwa lako silidzalowanso, ndipo mwezi wako sudzapitanso kumdima. Pakuti kwa iwe, Yehova adzakhala kuwala kosatha mpaka kalekale,+ ndipo masiku ako olira adzakhala atatha.+

  • Chivumbulutso 22:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Komanso, usiku sudzakhalakonso.+ Sadzafunikiranso kuwala kwa nyale kapena kwa dzuwa, chifukwa Yehova Mulungu adzawaunikira.+ Ndipo adzalamulira monga mafumu kwamuyaya.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena