Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 107:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Amasandutsa mitsinje kukhala chipululu,+

      Ndiponso akasupe a madzi kukhala malo opanda madzi.+

  • Yesaya 37:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndithu ineyo ndidzakumba zitsime ndi kumwa madzi,

      Ndidzaumitsa ndi mapazi anga ngalande zonse zamadzi za mtsinje wa Nailo+ wa ku Iguputo.’+

  • Yesaya 44:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ndine amene ndikuuza madzi akuya kuti, ‘Iphwa ndipo mitsinje yako yonse ndidzaiumitsa.’+

  • Yesaya 50:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 N’chifukwa chiyani nditabwera sindinapeze aliyense?+ N’chifukwa chiyani nditaitana palibe amene anayankha?+ Kodi dzanja langa lafupika kwambiri moti silingathe kuwombola,+ kapena kodi mwa ine mulibe mphamvu zopulumutsira? Inetu ndimaumitsa nyanja+ pongoidzudzula chabe.+ Mitsinje ndimaisandutsa chipululu.+ Nsomba zake zimanunkha chifukwa chakuti mulibe madzi ndipo zimafa ndi ludzu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena