2 Mafumu 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndithu ineyo ndidzakumba zitsime ndi kumwa madzi achilendo,Ndidzaumitsa ndi mapazi anga ngalande zonse zamadzi za mtsinje wa Nailo wa ku Iguputo.’+ Yesaya 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mitsinje idzanunkha. Ngalande za ku Iguputo zochokera mumtsinje wa Nailo zidzaphwa ndipo zidzauma.+ Bango+ ndi udzu* zidzafota.
24 Ndithu ineyo ndidzakumba zitsime ndi kumwa madzi achilendo,Ndidzaumitsa ndi mapazi anga ngalande zonse zamadzi za mtsinje wa Nailo wa ku Iguputo.’+
6 Mitsinje idzanunkha. Ngalande za ku Iguputo zochokera mumtsinje wa Nailo zidzaphwa ndipo zidzauma.+ Bango+ ndi udzu* zidzafota.