Ekisodo 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Poona kuti sakuthanso kum’bisa,+ anatenga kabokosi kagumbwa* n’kukamata phula.+ Kenako anaikamo mwanayo n’kukasiya kabokosiko pakati pa mabango+ m’mphepete mwa mtsinje wa Nailo. Yobu 40:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Imagona pansi pa mitengo yaminga,Pamalo obisika m’mabango+ ndi m’madambo.+
3 Poona kuti sakuthanso kum’bisa,+ anatenga kabokosi kagumbwa* n’kukamata phula.+ Kenako anaikamo mwanayo n’kukasiya kabokosiko pakati pa mabango+ m’mphepete mwa mtsinje wa Nailo.