Genesis 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Udzipangire chingalawa cha mtengo wa mnjale.+ Uchigawe zipindazipinda, ndipo uchimate ndi phula+ mkati ndi kunja komwe. Genesis 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako, mafumu a Sodomu ndi Gomora+ anayamba kuthawa. Koma chigwa cha Sidimu+ chinali ndi maenje aphula+ ambirimbiri, choncho iwo pothawa anali kugwera m’maenje amenewo. Amene anatsala anathawira kudera lamapiri.+
14 Udzipangire chingalawa cha mtengo wa mnjale.+ Uchigawe zipindazipinda, ndipo uchimate ndi phula+ mkati ndi kunja komwe.
10 Kenako, mafumu a Sodomu ndi Gomora+ anayamba kuthawa. Koma chigwa cha Sidimu+ chinali ndi maenje aphula+ ambirimbiri, choncho iwo pothawa anali kugwera m’maenje amenewo. Amene anatsala anathawira kudera lamapiri.+