Genesis 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako anauzana kuti: “Tiyeni tiumbe njerwa tiziotche.” Atatero, anayamba kumanga ndi njerwa, n’kumagwiritsa ntchito phula ngati matope omangira.+ Ekisodo 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Poona kuti sakuthanso kum’bisa,+ anatenga kabokosi kagumbwa* n’kukamata phula.+ Kenako anaikamo mwanayo n’kukasiya kabokosiko pakati pa mabango+ m’mphepete mwa mtsinje wa Nailo.
3 Kenako anauzana kuti: “Tiyeni tiumbe njerwa tiziotche.” Atatero, anayamba kumanga ndi njerwa, n’kumagwiritsa ntchito phula ngati matope omangira.+
3 Poona kuti sakuthanso kum’bisa,+ anatenga kabokosi kagumbwa* n’kukamata phula.+ Kenako anaikamo mwanayo n’kukasiya kabokosiko pakati pa mabango+ m’mphepete mwa mtsinje wa Nailo.