Machitidwe 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mfumu imeneyi inagwiritsa ntchito ulamuliro wake molakwika pofuna kuzunza anthu a fuko lathu,+ ndipo mwankhanza inachititsa makolo athuwo kutaya makanda awo, kuti asakhale ndi moyo.+
19 Mfumu imeneyi inagwiritsa ntchito ulamuliro wake molakwika pofuna kuzunza anthu a fuko lathu,+ ndipo mwankhanza inachititsa makolo athuwo kutaya makanda awo, kuti asakhale ndi moyo.+