2 Mafumu 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndithu ineyo ndidzakumba zitsime ndi kumwa madzi achilendo,Ndidzaumitsa ndi mapazi anga ngalande zonse zamadzi za mtsinje wa Nailo wa ku Iguputo.’+ Yesaya 37:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndithu ineyo ndidzakumba zitsime ndi kumwa madzi,Ndidzaumitsa ndi mapazi anga ngalande zonse zamadzi za mtsinje wa Nailo+ wa ku Iguputo.’+
24 Ndithu ineyo ndidzakumba zitsime ndi kumwa madzi achilendo,Ndidzaumitsa ndi mapazi anga ngalande zonse zamadzi za mtsinje wa Nailo wa ku Iguputo.’+
25 Ndithu ineyo ndidzakumba zitsime ndi kumwa madzi,Ndidzaumitsa ndi mapazi anga ngalande zonse zamadzi za mtsinje wa Nailo+ wa ku Iguputo.’+