Yesaya 46:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Beli+ wawerama+ ndipo Nebo wagwada. Mafano awo+ akhala katundu wa nyama zakutchire ndi wa nyama zoweta. Mafanowo angokhala katundu wolemera kwa nyama zotopa. Yeremiya 51:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 “Chotero masiku adzafika,” watero Yehova, “ndipo ndidzalanga zifaniziro zake zogoba.+ M’dziko lake lonse anthu obayidwa adzakhala akubuula.”+ Danieli 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakumwa vinyoyo, iwo anali kutamanda milungu yagolide, yasiliva, yamkuwa, yachitsulo, yamitengo ndi yamiyala.+
46 Beli+ wawerama+ ndipo Nebo wagwada. Mafano awo+ akhala katundu wa nyama zakutchire ndi wa nyama zoweta. Mafanowo angokhala katundu wolemera kwa nyama zotopa.
52 “Chotero masiku adzafika,” watero Yehova, “ndipo ndidzalanga zifaniziro zake zogoba.+ M’dziko lake lonse anthu obayidwa adzakhala akubuula.”+
4 Pakumwa vinyoyo, iwo anali kutamanda milungu yagolide, yasiliva, yamkuwa, yachitsulo, yamitengo ndi yamiyala.+