Maliro 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mdani watambasula dzanja lake n’kutenga zinthu+ zake zonse zabwino.Yerusalemu waona mitundu ina itabwera ndi kulowa m’malo ake opatulika,+Mitundu imene munalamula kuti isalowe mumpingo wanu.
10 Mdani watambasula dzanja lake n’kutenga zinthu+ zake zonse zabwino.Yerusalemu waona mitundu ina itabwera ndi kulowa m’malo ake opatulika,+Mitundu imene munalamula kuti isalowe mumpingo wanu.