Ezekieli 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Lupangalo layesedwa kuti aone ngati lili lakuthwa.+ Kodi chidzachitike n’chiyani ngati lupangalo likukana ndodo yachifumu?+ Ndodoyo sidzapitiriza kukhalapo,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
13 Lupangalo layesedwa kuti aone ngati lili lakuthwa.+ Kodi chidzachitike n’chiyani ngati lupangalo likukana ndodo yachifumu?+ Ndodoyo sidzapitiriza kukhalapo,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.