Yeremiya 39:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zitatero mfumu ya Babulo inapha+ ana aamuna a Zedekiya ku Ribila, Zedekiyayo akuona.+ Inaphanso akuluakulu onse a ku Yuda.+ Ezekieli 21:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Chotsa nduwira* ndipo vula chisoti chachifumu.+ Zinthu zasintha tsopano.+ Kweza munthu wotsika+ ndipo tsitsa munthu wokwezeka.+
6 Zitatero mfumu ya Babulo inapha+ ana aamuna a Zedekiya ku Ribila, Zedekiyayo akuona.+ Inaphanso akuluakulu onse a ku Yuda.+
26 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Chotsa nduwira* ndipo vula chisoti chachifumu.+ Zinthu zasintha tsopano.+ Kweza munthu wotsika+ ndipo tsitsa munthu wokwezeka.+