30 Yehova wanena kuti: “Ine ndikupereka Farao Hofira, mfumu ya Iguputo,+ m’manja mwa adani ake ndiponso m’manja mwa ofuna moyo wake,+ monga mmene ndinaperekera Zedekiya mfumu ya Yuda m’manja mwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo, mdani wa Zedekiyayo amene akufunanso moyo wake.”’”+