2 Mafumu 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo anapha ana a Zedekiya iye akuona,+ kenako Zedekiyayo anam’chititsa khungu.+ Atatero anamumanga ndi maunyolo amkuwa+ n’kupita naye ku Babulo.+ Ezekieli 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako moto unatuluka m’ndodo yake+ n’kunyeketsa nthambi zake ndi zipatso zake, ndipo mtengowo unalibenso ndodo yolimba yachifumu.+ “‘Imeneyi ndi nyimbo yoimba polira ndipo idzakhala nyimbo yotchuka.’”+
7 Iwo anapha ana a Zedekiya iye akuona,+ kenako Zedekiyayo anam’chititsa khungu.+ Atatero anamumanga ndi maunyolo amkuwa+ n’kupita naye ku Babulo.+
14 Kenako moto unatuluka m’ndodo yake+ n’kunyeketsa nthambi zake ndi zipatso zake, ndipo mtengowo unalibenso ndodo yolimba yachifumu.+ “‘Imeneyi ndi nyimbo yoimba polira ndipo idzakhala nyimbo yotchuka.’”+