Oweruza 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo kamtengo kamingako kanauza mitengoyo kuti, ‘Ngati mukunenadi zoona kuti mukufuna kundidzoza kuti ndikhale mfumu, bwerani mubisale mumthunzi wanga.+ Koma ngati si choncho, moto+ utuluke mwa ine ndi kunyeketsa mikungudza+ ya ku Lebanoni.’+ 2 Mafumu 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zimene zinachitika ku Yerusalemu ndi ku Yuda zinakwiyitsa+ kwambiri Yehova ndipo anawachotsa pamaso pake.+ Kenako Zedekiya anapandukira mfumu ya Babulo.+
15 Pamenepo kamtengo kamingako kanauza mitengoyo kuti, ‘Ngati mukunenadi zoona kuti mukufuna kundidzoza kuti ndikhale mfumu, bwerani mubisale mumthunzi wanga.+ Koma ngati si choncho, moto+ utuluke mwa ine ndi kunyeketsa mikungudza+ ya ku Lebanoni.’+
20 Zimene zinachitika ku Yerusalemu ndi ku Yuda zinakwiyitsa+ kwambiri Yehova ndipo anawachotsa pamaso pake.+ Kenako Zedekiya anapandukira mfumu ya Babulo.+