Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 36:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kuwonjezera pamenepo, Zedekiya anapandukira Mfumu Nebukadinezara+ yomwe inali itamulumbiritsa kwa Mulungu,+ ndipo anapitiriza kuumitsa khosi lake ndi mtima wake+ kuti asabwerere kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli.

  • Yeremiya 27:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Zedekiya+ mfumu ya Yuda ndinamuuza mawu onsewa+ kuti: “Ikani makosi anu m’goli la mfumu ya Babulo ndi kuitumikira. Mutumikire mfumuyo ndi anthu ake, kuti mukhalebe ndi moyo.+

  • Yeremiya 38:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pamenepo Yeremiya anauza Zedekiya kuti: “Yehova Mulungu wa makamu,+ Mulungu wa Isiraeli,+ wanena kuti, ‘Mukadzipereka kwa akalonga a mfumu ya Babulo,+ mudzakhalabe ndi moyo ndipo mzinda uwu sadzautentha, komanso inuyo ndi banja lanu mudzakhalabe ndi moyo.+

  • Ezekieli 17:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma iye anapandukira+ mfumuyo potumiza amithenga ku Iguputo kuti dziko la Iguputo limupatse mahatchi*+ ndi khamu la anthu. Kodi zinthu zidzamuyendera bwino? Kodi munthu amene akuchita zinthu zimenezi ndiponso amene akuphwanya pangano adzapulumuka? Kodi iye adzapulumukadi?’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena