Miyambo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mboni yonama sidzalephera kulangidwa,+ ndipo wolankhula mabodza sadzapulumuka.+ Yeremiya 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ndipo Zedekiya mfumu ya Yuda sadzapulumuka m’manja mwa Akasidi, pakuti adzaperekedwa ndithu m’manja mwa mfumu ya Babulo moti adzalankhulana ndi kuonana maso ndi maso ndi mfumuyo?”’+
4 ndipo Zedekiya mfumu ya Yuda sadzapulumuka m’manja mwa Akasidi, pakuti adzaperekedwa ndithu m’manja mwa mfumu ya Babulo moti adzalankhulana ndi kuonana maso ndi maso ndi mfumuyo?”’+