Yeremiya 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu amene adzakhalabe mumzindawu adzafa ndi lupanga, njala yaikulu ndiponso mliri.+ Koma amene adzatuluka ndi kugwidwa ndi Akasidi amene akuzungulirani adzakhala ndi moyo. Iwo adzapulumutsa moyo wawo.”’+ Yeremiya 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zedekiya+ mfumu ya Yuda ndinamuuza mawu onsewa+ kuti: “Ikani makosi anu m’goli la mfumu ya Babulo ndi kuitumikira. Mutumikire mfumuyo ndi anthu ake, kuti mukhalebe ndi moyo.+
9 Anthu amene adzakhalabe mumzindawu adzafa ndi lupanga, njala yaikulu ndiponso mliri.+ Koma amene adzatuluka ndi kugwidwa ndi Akasidi amene akuzungulirani adzakhala ndi moyo. Iwo adzapulumutsa moyo wawo.”’+
12 Zedekiya+ mfumu ya Yuda ndinamuuza mawu onsewa+ kuti: “Ikani makosi anu m’goli la mfumu ya Babulo ndi kuitumikira. Mutumikire mfumuyo ndi anthu ake, kuti mukhalebe ndi moyo.+