2 Mafumu 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zimene zinachitika ku Yerusalemu ndi ku Yuda zinakwiyitsa+ kwambiri Yehova ndipo anawachotsa pamaso pake.+ Kenako Zedekiya anapandukira mfumu ya Babulo.+ 2 Mbiri 36:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuwonjezera pamenepo, Zedekiya anapandukira Mfumu Nebukadinezara+ yomwe inali itamulumbiritsa kwa Mulungu,+ ndipo anapitiriza kuumitsa khosi lake ndi mtima wake+ kuti asabwerere kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli. Yeremiya 52:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zimene zinachitika ku Yerusalemu ndi ku Yuda zinakwiyitsa kwambiri Yehova ndipo anawachotsa pamaso pake.+ Kenako Zedekiya anapandukira mfumu ya Babulo.+ Ezekieli 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘“Kenako kunabwera chiwombankhanga china chachikulu+ chokhala ndi mapiko aakulu anthenga zikuluzikulu.+ Ndiyeno mwanjala, mtengo wa mpesawo unatambasula mizu yake ndi nthambi zake kuchokera pamene unabzalidwa kukafika pamene panali chiwombankhangacho+ kuti chithirire mtengowo.+
20 Zimene zinachitika ku Yerusalemu ndi ku Yuda zinakwiyitsa+ kwambiri Yehova ndipo anawachotsa pamaso pake.+ Kenako Zedekiya anapandukira mfumu ya Babulo.+
13 Kuwonjezera pamenepo, Zedekiya anapandukira Mfumu Nebukadinezara+ yomwe inali itamulumbiritsa kwa Mulungu,+ ndipo anapitiriza kuumitsa khosi lake ndi mtima wake+ kuti asabwerere kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli.
3 Zimene zinachitika ku Yerusalemu ndi ku Yuda zinakwiyitsa kwambiri Yehova ndipo anawachotsa pamaso pake.+ Kenako Zedekiya anapandukira mfumu ya Babulo.+
7 “‘“Kenako kunabwera chiwombankhanga china chachikulu+ chokhala ndi mapiko aakulu anthenga zikuluzikulu.+ Ndiyeno mwanjala, mtengo wa mpesawo unatambasula mizu yake ndi nthambi zake kuchokera pamene unabzalidwa kukafika pamene panali chiwombankhangacho+ kuti chithirire mtengowo.+