Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 24:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Zimene zinachitika ku Yerusalemu ndi ku Yuda zinakwiyitsa+ kwambiri Yehova ndipo anawachotsa pamaso pake.+ Kenako Zedekiya anapandukira mfumu ya Babulo.+

  • 2 Mbiri 36:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kuwonjezera pamenepo, Zedekiya anapandukira Mfumu Nebukadinezara+ yomwe inali itamulumbiritsa kwa Mulungu,+ ndipo anapitiriza kuumitsa khosi lake ndi mtima wake+ kuti asabwerere kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli.

  • Ezekieli 17:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma iye anapandukira+ mfumuyo potumiza amithenga ku Iguputo kuti dziko la Iguputo limupatse mahatchi*+ ndi khamu la anthu. Kodi zinthu zidzamuyendera bwino? Kodi munthu amene akuchita zinthu zimenezi ndiponso amene akuphwanya pangano adzapulumuka? Kodi iye adzapulumukadi?’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena