-
Oweruza 9:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Kamtengo kamingako kanauza mitengoyo kuti, ‘Ngati mukufunadi kundidzoza kuti ndikhale mfumu yanu, bwerani mubisale mumthunzi wanga. Koma ngati si choncho, moto utuluke mwa ine nʼkuwotcha mikungudza ya ku Lebanoni.’
-