Oweruza 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo kamtengo kamingako kanauza mitengoyo kuti, ‘Ngati mukunenadi zoona kuti mukufuna kundidzoza kuti ndikhale mfumu, bwerani mubisale mumthunzi wanga.+ Koma ngati si choncho, moto+ utuluke mwa ine ndi kunyeketsa mikungudza+ ya ku Lebanoni.’+ Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:15 Nsanja ya Olonda,2/15/2008, tsa. 9
15 Pamenepo kamtengo kamingako kanauza mitengoyo kuti, ‘Ngati mukunenadi zoona kuti mukufuna kundidzoza kuti ndikhale mfumu, bwerani mubisale mumthunzi wanga.+ Koma ngati si choncho, moto+ utuluke mwa ine ndi kunyeketsa mikungudza+ ya ku Lebanoni.’+