Nehemiya 9:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Zokolola za m’dzikoli zachulukira+ mafumu+ amene mwatiikira chifukwa cha machimo athu.+ Iwo akulamulira matupi athu komanso ziweto zathu mmene akufunira, ndipo tili pamavuto aakulu.+ Ezekieli 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngakhale kuti anatambasula dzanja lake+ povomereza lumbiro, iye wanyoza lumbiro+ limenelo mwa kuphwanya pangano. Iye wachita zinthu zonsezi ndipo sadzapulumuka.”’+ Ezekieli 21:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Chotsa nduwira* ndipo vula chisoti chachifumu.+ Zinthu zasintha tsopano.+ Kweza munthu wotsika+ ndipo tsitsa munthu wokwezeka.+
37 Zokolola za m’dzikoli zachulukira+ mafumu+ amene mwatiikira chifukwa cha machimo athu.+ Iwo akulamulira matupi athu komanso ziweto zathu mmene akufunira, ndipo tili pamavuto aakulu.+
18 Ngakhale kuti anatambasula dzanja lake+ povomereza lumbiro, iye wanyoza lumbiro+ limenelo mwa kuphwanya pangano. Iye wachita zinthu zonsezi ndipo sadzapulumuka.”’+
26 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Chotsa nduwira* ndipo vula chisoti chachifumu.+ Zinthu zasintha tsopano.+ Kweza munthu wotsika+ ndipo tsitsa munthu wokwezeka.+