Mateyu 5:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Tangotsimikizani kuti mukati Inde akhaledi Inde, ndipo mukati Ayi akhaledi Ayi,+ pakuti mawu owonjezera pamenepa achokera kwa woipayo.+ Aroma 1:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 osazindikira,+ osasunga mapangano,+ opanda chikondi chachibadwa+ ndiponso opanda chifundo.+
37 Tangotsimikizani kuti mukati Inde akhaledi Inde, ndipo mukati Ayi akhaledi Ayi,+ pakuti mawu owonjezera pamenepa achokera kwa woipayo.+