Miyambo 14:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Chilungamo chimakweza mtundu wa anthu,+ koma tchimo limachititsa manyazi mitundu ya anthu.+ Yesaya 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Maonekedwe a nkhope zawo akuwachitira umboni wotsutsana nawo,+ ndipo anthuwo akunena za tchimo lawo lofanana ndi la Sodomu.+ Iwo sanalibise. Tsoka kwa iwo, chifukwa adzibweretsera mavuto.+ Yesaya 59:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti zolakwa zathu zachuluka pamaso panu,+ ndipo tchimo lathu lililonse likupereka umboni wotsutsana nafe.+ Pakuti zolakwa zathu zili pa ife, ndipo zochimwa zathu tikuzidziwa bwino.+
9 Maonekedwe a nkhope zawo akuwachitira umboni wotsutsana nawo,+ ndipo anthuwo akunena za tchimo lawo lofanana ndi la Sodomu.+ Iwo sanalibise. Tsoka kwa iwo, chifukwa adzibweretsera mavuto.+
12 Pakuti zolakwa zathu zachuluka pamaso panu,+ ndipo tchimo lathu lililonse likupereka umboni wotsutsana nafe.+ Pakuti zolakwa zathu zili pa ife, ndipo zochimwa zathu tikuzidziwa bwino.+