Yesaya 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kodi mumenyedwanso pati+ mmene mukupitiriza kupandukamu?+ Mutu wanu uli ndi zilonda zokhazokha, ndipo mtima wanu wafooka.+ Ezekieli 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anapandukira zigamulo zanga pochita zoipa zoposa za mitundu ya anthuwo.+ Anapandukiranso malamulo anga kuposa mayiko amene amuzungulira, pakuti iye anakana zigamulo zanga ndipo sanayende m’malamulo anga.’+ 1 Atesalonika 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 amene anapha ngakhale Ambuye Yesu+ ndi aneneri+ ndi kuzunzanso ifeyo.+ Ndipo iwo sakukondweretsa Mulungu, koma akutsekereza zinthu zopindulitsa anthu onse.
5 Kodi mumenyedwanso pati+ mmene mukupitiriza kupandukamu?+ Mutu wanu uli ndi zilonda zokhazokha, ndipo mtima wanu wafooka.+
6 Iye anapandukira zigamulo zanga pochita zoipa zoposa za mitundu ya anthuwo.+ Anapandukiranso malamulo anga kuposa mayiko amene amuzungulira, pakuti iye anakana zigamulo zanga ndipo sanayende m’malamulo anga.’+
15 amene anapha ngakhale Ambuye Yesu+ ndi aneneri+ ndi kuzunzanso ifeyo.+ Ndipo iwo sakukondweretsa Mulungu, koma akutsekereza zinthu zopindulitsa anthu onse.