Deuteronomo 32:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yesuruni*+ atayamba kunenepa, anayamba kupanduka.+Iwe wanenepa, wakulupala, wakhuta mopitirira muyezo.+Pamenepo iye anasiya Mulungu amene anam’panga,+Ndi kunyoza Thanthwe+ la chipulumutso chake. 2 Mafumu 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo anapitiriza kuyenda motsatira malamulo+ a mitundu imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli, ndiponso motsatira malamulo amene mafumu a Isiraeli anapanga okha. Ezekieli 16:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Iwe sikuti unangoyenda chabe m’njira zawo ndiponso sikuti unangochita zinthu motsatira zinthu zawo zonyansa,+ koma m’nthawi yochepa unayamba kuchita zinthu zoipa kwambiri kuposa iwowo m’njira zako zonse.+
15 Yesuruni*+ atayamba kunenepa, anayamba kupanduka.+Iwe wanenepa, wakulupala, wakhuta mopitirira muyezo.+Pamenepo iye anasiya Mulungu amene anam’panga,+Ndi kunyoza Thanthwe+ la chipulumutso chake.
8 Iwo anapitiriza kuyenda motsatira malamulo+ a mitundu imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli, ndiponso motsatira malamulo amene mafumu a Isiraeli anapanga okha.
47 Iwe sikuti unangoyenda chabe m’njira zawo ndiponso sikuti unangochita zinthu motsatira zinthu zawo zonyansa,+ koma m’nthawi yochepa unayamba kuchita zinthu zoipa kwambiri kuposa iwowo m’njira zako zonse.+